current location : Lyricf.com
/
Songs
/
Pemphera nthawi ya m’mawa [English translation]
Pemphera nthawi ya m’mawa [English translation]
turnover time:2024-12-24 13:36:44
Pemphera nthawi ya m’mawa [English translation]

Pemphera nthawi ya m’mawa,

Pemphera nthawi yamasana.

Permphera nthawi yamadzulo,

Pemphera m’mtima.

Ayankha nthawi ya m’mawawa

Ayankha nthawi yamasana.

Ayankha nthawi yamadzulo

Pemphera mumtima

Angathe nthawi ya m’mawa

Angathe nthawi yamasana.

Angathe nthawi yamadzulo

Konzeka mumtima

Comments
Welcome to Lyricf comments! Please keep conversations courteous and on-topic. To fosterproductive and respectful conversations, you may see comments from our Community Managers.
Sign up to post
Sort by
Show More Comments
Malawi Folk
  • country:Malawi
  • Languages:Chewa
  • Genre:Folk
  • Wiki:https://en.wikipedia.org/wiki/Music_of_Malawi
Malawi Folk
Latest update
Copyright 2023-2024 - www.lyricf.com All Rights Reserved