Ndidzaimbira Ambuye wanga
Masiku onse a moyo wanga
(REF:)
Moyo wanga
Masiku a moyo wanga
Ndidzam’tamanda Ambuye wanga....
Ndidzam’gwadira Ambuye wanga...